Mmmmmh enikhei músic Kapa eni
O love you ndiwe moyo wanga uli welo udzakhala nkaziwanga Poti mwini wantimawanaga ndiweyo ukhale nane paliponse offcouse eya ndimanva thank you nonse ondikonda Finita onandipanga sapote!! Upanda iwe sinalikanthu pepana kundiyendela kumabwelako kwathu abuye udziwa chilichonse akuyanganile.