(verse 1)
Anthu akuvutika m'banja
Ankapita koyenda
Amaonako chimwemwe
Akafoka panyumba, mapokoso okhaokha
Koma ine ndili ndi mwayi
(chorus)
Iwe febe ndimakukonda
Chikondi chako ngati madzi
Madzi ozizira mu nthawi yotentha
Chili ngati nyali mu mdima
Umanditonthoza nthawi zonsezi
(Verse 2)
Ndine munthu nthawi Zina ndimalakwa
Chimwemwe chako
Chimandipatsa chiyembekezo
Tili ndi tsogolo,
Tsogolo lowala
(Chorus)
Iwe febe ndimakukonda
Chikondi chako ngati madzi
Madzi ozizira mu nthawi yotentha
Chili ngati nyali mu mdima
Umanditonthoza nthawi zonse
.......