Is your boy rafick ndimakukonda oo verah oo verah ndiposindizakusiya ndiwe nkazi okongola!!! alo athu azika koma iwe ndiine tizienda kupita chisogolo. alole athu azinyoza koma iwe ndine tisamavele ooo ndiwewekha ndiwewekha verah oo verah!!! mulungu anatilumikizanisa mitima iwe ndine kut tikhale Thupi limozi tie tizipephela Kuti azitisungabendimoyo wautali ndimakukonda oo verah ooo verah ndipo sindizakusiya ndiwe nkazi okongo ndipo tisalole athu kuti apasule chikondi chanthu athu alipo ambili amakamba zaiwe ngati aanakufusila ndiiowo tie tisalole kuti athu ngat a simioni grant ndi anyongo asokoneze zaubale wathu tie tiseke makutu athu poti iwo kufusila kumawavuta iwo machidule ndiouma