Chorus
Mmm mama mama good bayi good bayi mama mmmm mama muuse mu mtendele. Mama zaubwino wanu tidzasimba mama mmmm mama timkakukondani ife mama mmmm. Mama lesiti in pisi mamaaaaa .mmmm mama
Verse
Mama inu munali wathu thuzi pozimila wathu moto monga dambo tinayesetsa kupulumutsa wanu moyo koma satana wakubani mwatisiya yathu miyoyo ili mu ululu wawukulu. Munali pathu pobisala lathu kholo la malangizo mdambo moto mozimila. Mama kudasila ife tikulila koma tikudziwa. Kuti Allah wanu. Mzimu. Wasunga. Moyo winawo tidzaonanaso
Chorus
Mmm mama mama good bayi good bayi mama mmmm mama muuse mu mtendele. Mama zaubwino wanu tidzasimba mama mmmm mama timkakukondani ife mama mmmm. Mama lesiti in pisi mamaaaaa .mmmm mama
Verse2
Mama lest in pisi mamaaaaa malangazo anu aja ndayamba kuwakumbuka ndipo kulila kwathu mkosalekeza maka tikakumbuka anu macheza munali munthu osasankha mtundu mayi odzala ndi mzelu zakuya mwayinu timapindulamo koma paja satana kwake. Ndikuba taonani lelo wanu moyo watenga. Mmmm tikukayika ngati wina mayi ngati inu kuno kwa makunula tidzamupezeso komabe mwayi. Mzati wathu ulipo madala. akudadila. Alipo tikupempha. Allah wawo moyo awapatse. Wamphavu. Ndi. Wautali chifukwa. Ndi. Okkawo amatha kucheleza alendoooo
Chorus
Mmm mama mama good bayi good bayi mama mmmm mama muuse mu mtendele. Mama zaubwino wanu tidzasimba mama mmmm mama timkakukondani ife mama mmmm. Mama lesiti in pisi mamaaaaa .mmmm mama