Chilombo chikamabwela tonse nkhawa
Ayeh ayeh nkhawa chitipweteka pweteka
Pwetekahh ayehaye pweteka
Chilombo chikamabwela tonse nkhawa
Ayeh ayeh nkhawa chitipweteka pweteka
Pwetekahh ayehaye pweteka
Ine nkhawa zandichulukila ndipulumutseni ine
Anthuwa anyanya atipweteka tipulumutseni ife
Angonenepa ndi zigawenga tipulumutseni ife
Mukapanda kutelo atipweteka tipulumutseni ife
Chilombo chikamabwela tonse nkhawa
Ayeh ayeh nkhawa chitipweteka pweteka
Pwetekahh ayehaye pweteka
Awa atipweteka pweteka tipulumutseni ife
Aye ayeh iyah ayeh ayei iyai iyai
Awa atipweteka pweteka tipulumutseni ife
Aye ayeh iyah ayeh ayei iyai