Introduction
Iyeee iyeee yeee is a Mr raisan ooooo qaisward iyeee iyeee
Ves 1
No matter kuti ndiwe ndani
Tinaziwana pati
Ndili Nawe uli name popopo
Isazakhala minyama
Kapena kunama Ayi Ku Uma
Uzakhale ndamene
Chorus
Tisungane iwe Ndi ine
Tikhalane popeza ngwaine
Suma aaaaa Suma iwe Suma
Suma aaaaa Suma oweee Suma
Bridge
Pokhala pa iwe
Ndipodekha pa ine
No matter what are you back
Suzatha and you can get well
Ves 2
Ndimakukonda
Koma sungavese
Ndimaziziwa
Koma sungapeze
Zikhale mwaiwe keep it
Sunganana iwe wadzuka
Ending
Thanks for Emmanuel production