Wandisiya popanda chifukwa ndipo sindiziwa kuti vuto
Langa ndichani ndatani ine kuti nkhani zachikondizi
Ndizingoliramo
Mwina mkutheka ndinalakwa chani maka maka
Ndiuzeni zoona ngati ili minyama ndimasuleni
Chonde
(Chorus)
Ndalira ndalira
Lero ndiuzeni
Ndalira ndalira