intro
uh-huh yeahhh
it's black volt
hook
danso ndiyomweyi
kuzomba kulibe ina
Lilongwe ndiya danso
danso ndiyomweyi
kuzomba kulibe ina
Lilongwe ndiya danso
verse 1
ndikakamba za danso ,danso ndimafilu
ndimava kukoma ndikamayimba danso
use wakuzomba uyambe waphuzila ,kuti ufike pa Lilongwe danso
mukumayimba piano ,kodi piano ndi danso?
akuti kuli afro danso kodi afro ndi danso?
mwapulusha sound ndi kukopeka kwanuku
hook
danso ndiyomweyi
kuzomba kulibe ina
Lilongwe ndiya danso
danso ndiyomweyi
kuzomba kulibe ina
Lilongwe ndiya danso
verse 2
Ku Zomba mwayamba liti danso
kuti muyambe kulankhula monyoza
Lilongwe ndiya danso kuchokela kale
Zomba isanakhale ,inakhalako ndi Lilongwe
so a winter charge ndindani kunyoza Lilongwe
uleke zachibwana uyambe school
ndayambisa challenge ya beat ndayimbayi
ngati ndiwe dolo ubweze diss yangayi
ndilibe nazo Kaya umanyamula Jimi
hook
danso ndiyomweyi
kuzomba kulibe ina
Lilongwe ndiya danso
danso ndiyomweyi
kuzomba kulibe ina
Lilongwe ndiya danso
outro
Lilongwe....ya danso
kasungu....ya danso
mzuzu....ya danso
mchinjiso ....iliko danso
dedza uko...ya danso